Posts

Showing posts from March, 2025

Death Announcement

Image
 IMFA NAYOSO, YATICHOSERASO NSANAMIRA! Modzi mwa anthu omwe anali omenyera ufulu Mdziko muno , Benni Longwe watisiya atadwala atadwala thenda yotupa mwendo kwa nthawi ndithu dzuro,pa chipatala Cha Makwasa ,Thyolo . Modzi mwa mwa yemwe anali mzawo ,a Bon Kalindo ati Azamukumbikira Longwe ngati munthu olimba mtima kwambiri  Wolemba: ALINAFE JONAS