Death Announcement
IMFA NAYOSO, YATICHOSERASO NSANAMIRA!
Modzi mwa anthu omwe anali omenyera ufulu Mdziko muno , Benni Longwe watisiya atadwala atadwala thenda yotupa mwendo kwa nthawi ndithu dzuro,pa chipatala Cha Makwasa ,Thyolo .
Modzi mwa mwa yemwe anali mzawo ,a Bon Kalindo ati Azamukumbikira Longwe ngati munthu olimba mtima kwambiri
Wolemba: ALINAFE JONAS

May his soul rest in peace 🌹 🕊️
ReplyDeleteMHS RIP
ReplyDeleteMHSRIP
ReplyDeleteMHSRIP
ReplyDeleteMHSRIP
ReplyDeleteMHSRIP
ReplyDelete